Ezra 5:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tidaŵafunsanso maina ao, kuti tikalemba maina a atsogoleri ao, tidzakudziŵitseni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tinawafunsanso maina ao, kukudziwitsani, kuti tilembere maina a anthu akuwatsogolera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tinawafunsanso mayina a atsogoleri awo, kuti tikalemba mayina atsogoleriwo tidzakudziwitseni kuti muwadziwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tinawafunsanso maina ao, kukudziwitsani, kuti tilembere maina a anthu akuwatsogolera.