Ezra 5:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe chaka choyamba cha ufumu wa Kirusi mfumu ya ku Babiloni, Kirusiyo adapanga lamulo lakuti Nyumba ya Mulunguyi imangidwenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma chaka choyamba cha Kirusi mfumu ya Babiloni, Kirusi mfumuyo analamulira kuti azimanga nyumba iyi ya Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komabe chaka choyamba cha Koresi, mfumu ya ku Babuloni, mfumu Koresiyo anapereka lamulo lakuti Nyumba ya Mulunguyi imangidwenso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma caka coyamba ca Koresi mfumu ya Babulo, Koresi mfumuyo analamulira kuti azimanga nyumba iyi ya Mulungu.