Ezra 5:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mfumuyo idamuuza kuti, “Tenga ziŵiyazi, ukaziike m'Nyumba ya Mulungu ya ku Yerusalemu, ndipo Nyumbayo imangidwenso pa maziko ake akale.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nati naye, Tenga zipangizo izi, kaziike m'Kachisi ali m'Yerusalemu, nimangidwe nyumba ya Mulungu pambuto pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono mfumuyo inamuwuza kuti, ‘Tenga ziwiyazi ukaziyike mʼNyumba ya Mulungu ku Yerusalemu. Ndipo Nyumba ya Mulunguyo ikamangidwenso pa maziko ake akale.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nati naye, Tenga zipangizo izi, kaziike m'Kacisi ali m'Yerusalemu, nimangidwe nyumba ya Mulungu pambuto pace.