Ezra 5:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Sesibazarayo adabwera, nayamba kumanga maziko a Nyumba ya Mulungu ku Yerusalemu. Kuyambira nthaŵi imeneyo mpaka tsopano yakhala ikumangidwa, ndipo siinathebe.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo anadza Sezibazara yemweyo namanga maziko a nyumba ya Mulungu ili m'Yerusalemu; ndipo kuyambira pomwepo kufikira tsopano ilinkumangidwa, koma siinatsirizike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Choncho Sesibazarayo anabwera ndi kumanga maziko a Nyumba ya Mulunguyo mu Yerusalemu. Kuyambira tsiku limenelo mpaka lero yakhala ikumangidwa ndipo sinathebe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo anadza Sezibazara yemweyo namanga maziko a nyumba ya Mulungu iri m'Yerusalemu; ndipo kuyambira pomwepo kufikira tsopano irimkumangidwa, koma siinatsirizike.