Ezra 5:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵafunsanso kuti, “Kodi anthu amene akumanga Nyumba imeneyiŵa, maina ao ndani?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanena naonso motere, Maina ao a anthu omanga chimangidwe ichi ndiwo ayani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anawafunsanso kuti, “Kodi anthu amene akumanga nyumbayi mayina awo ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanena naonso motere, Maina ao a anthu omanga cimangidwe ici ndiwo ayani?