Ezra 5:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nayi kalata yomwe Tatenai, bwanamkubwa wa dera la Patsidya pa Yufurate, ndiponso Setari-Bozenai ndi anzake, akazembe omwe anali m'chigawo cha Patsidya pa Yufurate, adatumiza kwa mfumu Dariusi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zolembedwa m'kalata amene Tatenai kazembe wa tsidya lino la mtsinjewo, ndi Setari-Bozenai, ndi anzake Afarisikai, okhala tsidya lino la mtsinje, anatumiza kwa Dariusi mfumu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyi ndi kalata imene Tatenai bwanamkubwa wa dera la patsidya pa Yufurate, ndiponso Setari-Bozenai ndi anzake, akazembe amene anali mʼchigawo cha patsidya pa Yufurate, anatumiza kwa mfumu Dariyo
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zolembedwa m'kalata amene Tatinai kazembe wa tsidya lino la mtsinjewo, ndi Setara Bozenai, ndi anzace Afarisikai, okhala tsidya lino la mtsinje, anatumiza kwa Dariyo mfumu,