Ezra 5:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono tidaŵafunsa atsogoleriwo kuti, ‘Kodi adakulamulani ndani kuti mumange Nyumba imeneyi ndi kutsiriza makoma ake?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo tinafunsa akulu aja ndi kutere nao, Anakulamulirani ndani kumanga nyumba iyi, ndi kutsiriza khoma ili?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo tinawafunsa atsogoleriwo kuti, “Anakulolezani kuti mumangenso Nyumbayi ndi kutsiriza makoma ake ndani?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo tinafunsa akulu aja ndi kutere nao, Anakulamulirani ndani kumanga nyumba iyi, ndi kutsiriza khoma ili?