Ezra 6:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimenezi zichitike kuti azipereka nsembe za fungo lokomera Mulungu Wakumwamba, ndi kuti anthuwo apempherere moyo wa mfumu ndi wa ana ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti apereke nsembe zonunkhira bwino kwa Mulungu wa Kumwamba, napempherere moyo wa mfumu ndi wa ana ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zikatero ndiye kuti azipereka nsembe za fungo lokomera Mulungu wakumwamba ndi kupempherera moyo wa mfumu ndi ana ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti apereke nsembe zonunkhira bwino kwa Mulungu wa Kumwamba, napempherere moyo wa mfumu ndi wa ana ace.