Ezra 6:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono potsata mau amene mfumu Dariusi adaalamula, Tatenai, bwanamkubwa wa dera la Patsidya pa Yufurate, Setari-Bozenai ndi anzao adachita mosamala kwambiri zimene mfumu Dariusi adaalamula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Tatenai kazembe wa tsidya lino la mtsinjewo, Setari-Bozenai, ndi anzao, popeza mfumu Dariusi adatumiza mau, anachita momwemo chofulumira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono potsata zomwe analamula mfumu Dariyo, Tatenai bwanamkubwa wa dera la Patsidya pa Yufurate, Setari-Bozenai ndi anzawo anatsatira mosamala kwambiri zimene mfumu Dariyo analamula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Tatinai kazembe wa tsidya lino la mtsinjewo, Setara Bozenai, ndi anzao, popeza mfumu Dariyo adatumiza mau, anacita momwemo cofulumira.