Ezra 6:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Aisraele, ndiye kuti ansembe, Alevi ndi anthu ena onse amene anali atabwerako ku ukapolo, adachita chikondwerero cha kupereka Nyumba ya Mulungu mwachimwemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ana a Israele, ansembe ndi Alevi, ndi ana otsala a ndende, anapereka nyumba iyi ya Mulungu mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Aisraeli, ansembe, Alevi ndi anthu ena onse amene anali atabwerako ku ukapolo, anachita chikondwerero chopereka Nyumba ya Mulungu mwachimwemwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ana a Israyeli, ansembe ndi Alevi, ndi ana otsala a ndende, anapereka nyumba iyi ya Mulungu mokondwera.