Ezra 6:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho adaŵakhazika ansembe ndi Alevi pa ntchito zao zotumikira Mulungu ku Yerusalemu, monga momwe zidalembedwera m'buku la Mose.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Naika ansembe m'magawo mwao, ndi Alevi m'magawidwe mwao, atumikire Mulungu wokhala ku Yerusalemu, monga mulembedwa m'buku la Mose.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anakhazikitsa ansembe ndi Alevi pa ntchito zawo zotumikira Mulungu mu Yerusalemu monga zinalembedwera mʼbuku la Mose.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Naika ansembe m'magawo mwao, ndi Alevi m'magawidwe mwao, atumikire Mulungu wokhala ku Yerusalemu, monga mulembedwa m'buku la Mose.