Ezra 6:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ku Ekibatana, likulu la dziko la Mediya, kudapezeka mpukutu m'mene mudaalembedwa kuti, “Chikumbutso.” Mau ake anali aŵa:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Napeza ku Ekibatana m'nyumba ya mfumu m'dera la Mediya, mpukutu, ndi m'menemo munalembedwa motere, chikhale chikumbutso:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ku Ekibatana, likulu la dera la Mediya, kunapezeka mpukutu mmene munalembedwa kuti, Chikumbutso:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Napeza ku Akimeta m'nyumba ya mfumu m'dera la Mediya, mpukutu, ndi m'menemo munalembedwa motere, cikhale cikumbutso: