Ezra 6:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ntchito iyi yomanga Nyumba ya Mulungu muileke. Mlekeni bwanamkubwa wa ku dera la Yuda ndiponso atsogoleri akumeneko kuti amangenso Nyumba ya Mulunguyo pamalo pake ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
lekani ntchito iyi ya Mulungu, osaivuta; kazembe wa Ayuda ndi akulu a Ayuda amange nyumba iyi ya Mulungu pambuto pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ntchito yomanga Nyumba ya Mulunguyi muyileke. Mulekeni bwanamkubwa wa Ayuda ndiponso akuluakulu a Ayuda kuti amangenso Nyumba ya Mulunguyo pamalo pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
lekani nchito iyi ya Mulungu, osaibvuta; kazembe wa Ayuda ndi akulu a Ayuda amange nyumba iyi ya Mulungu pambuto pace.