Ezra 7:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ndine, Arita-kisereksesi, mfumu ya mafumu, ndikulembera iwe Ezara, wansembe ndi mlembi wa malamulo a Mulungu Wakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Arita-kisereksesi mfumu ya mafumu kwa Ezara wansembe, mlembi wa lamulo la Mulungu wa Kumwamba, mtendere weniweni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndine Aritasasita, mfumu ya mafumu. Ndikulembera iwe Ezara wansembe ndi mlembi wa malamulo a Mulungu Wakumwamba. Malonje.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aritasasta mfumu ya mafumu kwa Ezara wansembe, mlembi wa lamulo la Mulungu wa Kumwamba, mtendere weni weni, ndi pa nthawi yakuti.