Ezra 7:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndalama zotsala muzigwiritse ntchito monga momwe inuyo ndi abale anu mungafunire malinga nkufuna kwa Mulungu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chilichonse chidzakomera iwe ndi abale ako kuchita nazo siliva ndi golide zotsala, ichi muchite monga mwa chifuniro cha Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndalama zotsala mudzagwiritse ntchito zimene inuyo ndi abale anu zikakukomerani malingana nʼkufuna kwa Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ciri conse cidzakomera iwe ndi abale ako kucita nazo siliva ndi golidi zotsala, ici mucite monga mwa cifuniro ca Mulungu wanu.