Ezra 7:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zonse zimene Mulungu Wakumwamba alamule, zichitike mwachangu ku Nyumba ya Mulungu Wakumwamba, kuwopa kuti mkwiyo wake ungayakire mfumu ndi dziko lake ndi ana ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilichonse Mulungu wa Kumwamba achilamulire chichitikire mwachangu nyumba ya Mulungu wa Kumwamba; pakuti padzakhaliranji mkwiyo pa ufumu wa mfumu ndi ana ake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chimene Mulungu Wakumwamba walamula, chichitike mosamalitsa ku Nyumba ya Mulungu Wakumwamba kuopa kuti mkwiyo wa Mulungu ungayakire mfumu, dziko lake ndi ana ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ciri conse Mulungu wa Kumwamba acilamulire cicitikire mwacangu nyumba ya Mulungu wa Kumwamba; pakuti padzakhaliranji mkwiyo pa ufumu wa mfumu ndi ana ace?