Ezra 7:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ezara adati, “Atamandike Chauta, Mulungu wa makolo athu, amene adaika nzeru zotere mu mtima wa mfumu, kuti apereke ulemu ku Nyumba ya Mulungu ya ku Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala Yehova Mulungu wa makolo athu, amene anaika chinthu chotere mu mtima wa mfumu, kukometsera nyumba ya Yehova ili ku Yerusalemu,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ezara anati atamandike Yehova, Mulungu wa makolo athu, amene wayika ichi mu mtima wa mfumu kuti alemekeze Nyumba ya Yehova ya ku Yerusalemu mʼnjira imeneyi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala Yehova Mulungu wa makolo athu, amene anaika cinthu cotere mu mtima wa mfumu, kukometsera nyumba ya Yehova iri ku Yerusalemu,