Ezra 8:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nawu mndandanda wa maina a atsogoleri a mabanja amene adabwera nane kuchokera ku Babiloni, pa nthaŵi ya ufumu wa Arita-kisereksesi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo akulu a nyumba za makolo ndi awa, ndi chibadwidwe cha iwo okwera nane limodzi kuchokera ku Babiloni, pokhala mfumu Arita-kisereksesi, ndi ichi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nawa mayina a atsogoleri a mabanja amene anabwera nane kuchokera ku Babuloni nthawi ya ulamuliro wa mfumu Aritasasita:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo akuru a nyumba za makolo ndi awa, ndi cibadwidwe ca iwo okwera nane limodzi kucokera ku Babulo, pokhala mfumu Aritasasta, ndi ici: