Ezra 8:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Selomiti, mwana wa Yosofiya, wa fuko la Bani. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 160.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi wa ana a Selomiti, mwana wa Yosofiya; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Selomiti mwana wa Yosifiya wa fuko la Bani. Pamodzi ndi iyeyu panalinso anthu 160.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi wa ana a Selomiti, mwana wa Yosifiya; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu makumi asanu ndi limodzi.