Ezra 8:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zekariya, mwana wa Bebai, wa fuko la Bebai. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 28.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi wa ana a Bebai, Zekariya mwana wa Bebai; ndi pamodzi naye amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zekariya, mwana wa Bebai wa fuko la Babai. Pamodzi naye analembedwanso anthu 28.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi wa ana a Bebai, Zekariya mwana wa Bebai; ndi pamodzi naye amuna makumi awiri mphambu asanu ndi atatu.