Ezra 8:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yohanani, mwana wa Hakatani, wa fuko la Azigadi. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 110.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi wa ana a Azigadi, Yohanani mwana wa Hakatani; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu khumi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yohanani, mwana wa Hakatani wa fuko la Azigadi. Pamodzi naye panalinso anthu 110.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi wa ana a Azigadi, Yohanana mwana wa Hakatana; ndi pamodzi naye amuna zana limodzi mphambu khumi limodzi.