Ezra 8:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atsogoleri a fuko la Adonikamu, anthu amene adabwera pambuyo pake, anali Elifeleti, Yeiyele ndi Semaya, ndipo pamodzi ndi iwowo panali anthu 60.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi a ana otsiriza a Adonikamu, maina ao ndiwo Elifeleti, Yeiyele, ndi Semaya; ndi pamodzi nao amuna makumi asanu ndi limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atsogoleri a fuko la Adonikamu, anthu amene anabwera pambuyo pake mayina awo anali Elifeleti, Yeiyeli ndi Semaya. Pamodzi ndi iwowa panalinso anthu 60.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi a ana otsiriza a Adonikmnu, maina ao ndiwo Elifeleti, Yeueli, ndi Semaya; ndi pamodzi nao amuna makumi asanu ndi limodzi.