Ezra 8:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onsewo ndidaŵasonkhanitsa ku mtsinje umene umafika mpaka ku mudzi wa Ahava, ndipo kumeneko tidagona m'zithando masiku atatu. Pamene ndinkayang'ana anthu ndi ansembe, ndidapeza kuti ana a Levi palibe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinawasonkhanitsa ku mtsinje wopita ku Ahava, ndi komweko tinakhala m'misasa masiku atatu; ndipo ndinapenyerera anthu ndi ansembe, koma sindinapezapo wa ana a Levi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse ndinawasonkhanitsa ku mtsinje umene umapita mpaka ku Ahava, ndipo kumeneko tinagona mʼmisasa masiku atatu. Nditayangʼana pakati pa anthu ndi ansembe, ndinapeza kuti panalibe Alevi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinawasonkhanitsa ku mtsinje wopita ku Ahava, ndi komweko tinakhala m'misasa masiku atatu; ndipo ndinapenyerera anthu ndi ansembe, koma sindinapezapo wa ana a Levi.