Ezra 8:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatitumiziranso Hasabiya ndi Yeshaiya wa fuko la Merari, kudzanso achibale ake ndiponso ana ao, anthu makumi aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Hasabiya, ndi pamodzi naye Yesaya wa ana a Merari, abale ake ndi ana ao makumi awiri;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anatitumiziranso Hasabiya ndi Yesaiya wa fuko la Merari pamodzi ndi abale ake ndi adzukulu ake, anthu makumi awiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Hasabiya, ndi pamodzi naye Yesaya wa ana a Merari, abale ace ndi ana ao makumi awiri;