Ezra 8:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Panalinso atumiki a ku Nyumba ya Mulungu okwanira 220, amene Davide ndi nduna zake adaaŵasankha kuti azitumikira Alevi. Anthu onseŵa adalembedwa potsata maina ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi a Anetini, amene Davide ndi akalonga adapereka atumikire Alevi, Anetini mazana awiri mphambu makumi awiri, onsewo otchulidwa maina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Panalinso anthu ena 220 mwa anthu ogwira ntchito mʼNyumba ya Mulungu amene Davide ndi nduna zake anawasankha kuti azitumikira Alevi. Anthu onsewa analembedwa potsata mayina awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi a Anetini, amene Davide ndi akalonga adapereka atumikire Alevi, Anetini mazana awiri mphambu makumi awiri, onsewo ochulidwa maina.