Ezra 8:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nditaziyesa zonse, ndidaŵapatsa m'manja mwao siliva wa matani 22, ziŵiya zasiliva za makilogaramu 70, ndiponso golide wa makilogaramu 3,400,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinawayesera m'dzanja mwao matalente a siliva mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu, ndi zipangizo zasiliva matalente zana limodzi,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nditayeza zonse, ndinapereka mʼmanja mwawo, matani 22 asiliva, ziwiya zasiliva zolemera makilogalamu 70, ndiponso makilogalamu 3,400 a golide,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinawayesera m'dzanja mwao matalente a siliva mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu, ndi zipangizo zasiliva matalente zana limodzi,