Ezra 8:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mbale zagolide makumi aŵiri zolemera makilogaramu pafupi 8 ndi theka, ndiponso ziŵiya ziŵiri za mkuŵa wosalala wonyezemira bwino, zamtengowapatali wonga wa golide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi zikho zagolide makumi awiri za madariki chikwi chimodzi, ndi zipangizo ziwiri za mkuwa wabwino wonyezimira wokhumbika ngati golide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mbale zagolide makumi awiri zolemera makilogalamu asanu ndi atatu ndi theka ndiponso ziwiya ziwiri zamkuwa wosalala, wonyezimira bwino ngati golide wamtengowapatali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi zikho zagolidi makumi awiri za madariki cikwi cimodzi, ndi zipangizo ziwiri za mkuwa wabwino wonyezimira wokhumbika ngati golidi.