Ezra 8:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Hatusi, mwana wa Sekaniya, wa fuko la Davide. Zekariya, wa fuko la Parosi. Iyeyu adalembedwa pamodzi ndi anthu ena okwanira 150.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa ana a Sekaniya, wa ana a Parosi, Zekariya; ndi pamodzi naye, powawerenga monga mwa chibadwidwe chao, amuna zana limodzi mphambu makumi asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mwana wa Sekaniya wa fuko la Davide; Zekariya wa fuko la Parosi. Pamodzi ndi iyeyu panalembedwa anthu ena 150;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa ana a Sekaniya, wa ana a Parosi, Zekariya; ndi pamodzi naye, powawerenga monga mwa cibadwidwe cao, amuna zana limodzi mphambu makumi asanu.