Ezra 8:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Eliehoenai, mwana wa Zerahiya, wa fuko la Pahatimowabu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 200.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa ana a Pahatimowabu, Eliehoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Elihunai mwana wa Zerahiya, wa fuko la Pahati-Mowabu. Pamodzi ndi iyeyu panalinso anthu ena 400.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa ana a Pahati Moabu, Elihoenai mwana wa Zerahiya; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri.