Ezra 8:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sekaniya, mwana wa Yahaziele, wa fuko la Zatu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 300.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa ana a Sekaniya, mwana wa Yahaziele; ndi pamodzi naye amuna mazana atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sekaniya, mwana wa Yahazieli wa fuko la Zatu. Pamodzi ndi iyeyu panalembedwanso anthu 300.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa ana a Sekaniya, mwana wa Yahazieli; ndi pamodzi naye amuna mazana atatu.