Ezra 8:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ebedi, mwana wa Yonatani, wa fuko la Adini. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 50.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi wa ana a Adini, Ebedi mwana wa Yonatani; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ebedi, mwana wa Yonatani wa fuko la Adini. Pamodzi naye analembedwanso anthu ena makumi asanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi wa ana a Adini, Ebedi mwana wa Yonatani; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu.