Ezra 8:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yesaya, mwana wa Ataliya, wa fuko la Elamu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 70.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi wa ana a Elamu, Yesaya mwana wa Ataliya; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu ndi awiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yesaiya, mwana wa Ataliya wa fuko la Elamu. Pamodzi naye panali anthu ena 70.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi wa ana a Elamu, Yesaya mwana wa Ataliya; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu ndi awiri.