Ezra 8:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Obadiya, mwana wa Yehiyele, wa fuko la Yowabu. Pamodzi ndi iyeyo panali anthu 218.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wa ana a Yowabu, Obadiya mwana wa Yehiyele; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri mphambu khumi kudza asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Obadiya, mwana wa Yehieli wa fuko la Yowabu. Pamodzi naye panalinso anthu 218.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wa ana a Yoabu, Obadiya mwana wa Yehieli; ndi pamodzi naye amuna mazana awiri mphambu khumi kudza asanu ndi atatu.