Galatians 1:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkapambana anzanga ambiri a msinkhu wanga pochita zachiyuda, ndipo ndinali wachangu koposa potsata miyambo ya makolo athu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ndinawaposa ndi kutsogola mwa Chiyuda ambiri a msinkhu wanga mwa mtundu wanga, ndipo ndinakhala wachangu koposa pa miyambo ya makolo anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinkapambana Ayuda ambiri a msinkhu wanga pochita za Chiyuda, ndipo ndinali wachangu koposa pa miyambo ya makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ndinawaposa ndi kutsogola mwa Ciyuda ambiri a msinkhu wanga mwa mtundu wanga, ndipo ndinakhala wacangu koposa pa miyambo ya makolo anga.