Galatians 1:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono pamene adatsimikiza zondiwululira Mwana wake, kuti choncho ndikalalike Uthenga Wabwino wonena za Iye kwa anthu amene sali Ayuda, sindidapite kwa munthu aliyense kuti ndikapemphe nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti avumbulutse Mwana wake mwa ine, kuti ndimlalikire Iye mwa amitundu; pomwepo sindinafunsana ndi thupi ndi mwazi:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuvumbulutsa Mwana wake mwa ine, kuti ndikalalikire Khristuyo pakati pa anthu a mitundu ina, ine sindinapemphe nzeru kwa munthu aliyense.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti abvumbulutse Mwana wace mwa ine, kuti ndimlalikire iye mwa amitundu; pomwepo sindinafunsana ndi thupi ndi mwazi: