Galatians 1:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake ndidakafika ku madera a ku Siriya ndi a ku Silisiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene ndinadza kumbali za Siriya ndi Silisiya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake ndinapita ku Siriya ndi ku Kilikiya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo ndinadza ku mbali za Suriya ndi Kilikiya.