Galatians 1:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma chonsecho nkuti mipingo yachikhristu ya ku Yudeya isanandiwone ndi kundidziŵa bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ndinali wosadziwika nkhope yanga kwa Mipingo ya ku Yudeya ya mwa Khristu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sindimadziwika ndi nkhope ku mipingo ya ku Yudeya imene ili mwa Khristu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ndinali wosadziwika nkhope yanga kwa Mipingo ya ku Yudeya ya mwa Kristu;