Galatians 1:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inali itangomva mbiri chabe yakuti, “Munthu uja ankatizunza kaleyu, tsopano akulalika chikhulupiriro chimene kale lija ankayesetsa kuchiwononga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma analinkumva kokha, kuti, Iye wakutilondalonda ife kale, tsopano alalikira chikhulupirirocho adachipasula kale;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anangomva mbiri yokha yakuti, “Munthu amene poyamba anatizunza ife, tsopano akulalikira chikhulupiriro chimene iyeyo nthawi ina anafuna kuchiwononga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma analinkumva kokha, kuti, iye wakutilondalonda ife kale, tsopane alalikira cikhulupiriroco ada cipasula kale;