Galatians 1:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikudabwa kuti mukupatuka msangamsanga motere, kusiya Mulungu amene adakuitanani mwa kukoma mtima kwa Khristu, ndipo kuti mukutsata uthenga wabwino wina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndizizwa kuti msanga motere mulikupatuka kwa iye amene anakuitanani m'chisomo cha Khristu, kutsata Uthenga Wabwino wina;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndikudabwa kuti mukusiya mwamsangamsanga chotere Mulungu amene anakuyitanani mwachisomo cha Khristu ndipo mwatembenuka ndi kutsatira uthenga wina wosiyana,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndizizwa kuti msanga motere mulikutunsika kwa iye amene anakuitanani m'cisomo ca Kristu, kutsata uthenga wabwino wina;