Galatians 2:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene Petro adafika ku Antiokeya, ndidamtsutsa poyera, chifukwa adaapezeka wolakwadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene Kefa anadza ku Antiokeya ndinatsutsana naye pamaso pake, pakuti anatsutsika wolakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Petro atafika ku Antiokeya, ine ndinamudzudzula pa gulu chifukwa anapezeka wolakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene Kefa anadza ku Antiokeyandinatsutsana naye pamaso pace, pakuti anatsutsika wolakwa.