Galatians 2:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malamulo ndiwo adandizindikiritsa kuti ndiyenera kulekeratu kuŵadalira Malamulowo, ndipo kuti moyo wanga wonse uyenera kukhala wodalira Mulungu mwini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ine mwa lamulo ndafa kulamulo, kuti ndikhale ndi moyo kwa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pakuti pamene ndinayesera kutsatira lamulo, lamulolo linandionetsa kuti ndine wochimwa. Choncho ndinasiya kutsatira lamulo kuti ndikhale ndi moyo kwa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ine mwa lamulo ndafa ku lamulo, kuti ndikhale ndi moyo kwa Mulungu.