Galatians 2:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mnzanga uja, Tito, ngakhale ndi Mgriki, sadamkakamize kuti aumbalidwe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Komatu ngakhale Tito, amene anali ndi ine, ndiye Mgriki, sanamkakamiza adulidwe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu ngakhale Tito, amene anali nane sanakakamizidwe kuti achite mdulidwe, ngakhale iyeyo anali Mgriki.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Komatu ngakhale Tito, amene anali ndi ine, ndiye Mhelene, sanamkakamiza adulidwe;