Galatians 2:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sitidaŵagonjere mpang'ono pomwe, popeza kuti tinkafuna kukusungirani kwathunthu zoona za Uthenga Wabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma sitidawafumukira mowagonjera ngakhale ora limodzi; kuti choonadi cha Uthenga Wabwino chikhalebe ndi inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife sitinawagonjere ndi pangʼono pomwe, nʼcholinga chakuti choonadi cha Uthenga Wabwino chikhalebe ndi ife.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma sitidawafumukira mowagonjera ngakhale ora limodzi; kuti coonadi ca Uthenga Wabwino cikhalebe ndi inu.