Galatians 2:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti Mulungu yemweyo amene adagwira ntchito mwa Petro pomutuma ngati mtumwi kwa Ayuda, adagwiranso ntchito mwa ine, pondituma ngati mtumwi kwa anthu a mitundu ina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(pakuti Iye wakuchita mwa Petro kumtuma kwa odulidwa anachitanso mwa ine kundituma kwa amitundu);
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Mulungu, amene amagwira ntchito mu utumiki wa Petro monga mtumwi kwa Ayuda, amagwiranso ntchito mu utumiki wanga monga mtumiki kwa anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(pakuti iye wakucita mwa Petro kumtuma kwa odulidwa anacitanso mwa ine kundituma kwa amitundu);