Galatians 3:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Agalatiya opusa inu, adakulodzani ndani? Pamene tidakulalikirani Yesu Khristu, tidamuwonetsa poyera pamaso panu ngati wopachikidwa pa mtanda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani, inu amene Yesu Khristu anaonetsedwa pa maso panu, wopachikidwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani? Tinamuonetsa poyera pamaso panu Yesu Khristu monga wopachikidwa pa mtanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani, inu amene Kristu anaonetsedwa pa maso panu, wopacikidwa?