Galatians 3:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono tikati mkhalapakati, ndiye kuti pali anthu aŵiri. Koma Mulungu ali yekha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma nkhoswe siili ya mmodzi; koma Mulungu ali mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale zili chomwecho, mʼkhalapakati sayimira mbali imodzi yokha, koma Mulungu ndi mmodzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma nkhoswe siiri ya mmodzi; koma Mulungu ali mmodzi.