Galatians 3:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndiye kuti Malamulo a Mose amatsutsana ndi malonjezo a Mulungu? Mpang'ono pomwe. Anthu akadalandira malamulo otha kuŵapatsa moyo, pamenepo bwenzi atasanduka olungama kudzera mwa malamulowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo kodi chilamulo chitsutsana nao malonjezano a Mulungu? Msatero ai. Pakuti chikadapatsidwa chilamulo chakukhoza kuchitira moyo, chilungamo chikadachokera ndithu kulamulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ndiye kuti lamulo limatsutsana ndi malonjezo a Mulungu? Ayi. Nʼkosatheka! Pakuti ngati tikanapatsidwa malamulo opatsa moyo ndiye kuti mwa lamulo tikanakhala olungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo kodi cilamulo citsutsana nao malonjezano a Mulungu? Msatero ai. Pakuti cikadapatsidwa cilamulo eakukhoza kucitira moyo, cilungamo cikadacokera ndithu kulamulo.