Galatians 3:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chisanafike chikhulupirirochi, tinali ngati akaidi m'manja mwa Malamulo, kudikira kuti chikhulupiriro chimene chidaati chifikecho, chiwululidwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma chisanadze chikhulupiriro tinasungidwa pomvera lamulo otsekedwa kufikira chikhulupiriro chimene chikavumbulutsidwa bwinobwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikhulupiriro ichi chisanabwere, ife tinali mʼndende ya lamulo, otsekeredwa mpaka pamene chikhulupiriro chikanavumbulutsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma cisanadze cikhulupiriro tinasungidwa pomvera lamulo otsekedwa kufikira cikhulupiriro cimene cikabvumbulutsidwa bwino bwino.