Galatians 3:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati ndinu ake a Khristu, ndiye kuti ndinu ana a Abrahamu, oyenera kulandira zimene Mulungu adalonjeza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ngati muli a Khristu, muli mbeu ya Abrahamu, nyumba monga mwa lonjezano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati inu muli ake a Khristu, ndiye kuti ndinu mbewu ya Abrahamu, ndi olowamʼmalo molingana ndi lonjezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ngati muli a Kristu, muli mbeu ya Abrahamu, 7 nyumba monga mwa Lonjezano.