Galatians 3:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi mudalandira zonse zija pachabe? Sindikukhulupirira kuti mpachabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi mudamva zowawa zambiri zotere kwachabe? Ngatitu kwachabe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi munavutika kwambiri pachabe, ngati kunali kwachabedi?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi mudamva zowawa zambiri zotere kwacabe? ngatitu kwacabe.